Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yesu anayankha kuti: “Kodi usana suli ndi maola 12? Munthu akayenda masana+ palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.

  • 2 Petulo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa chifukwa chimenechi abale, chitani chilichonse chotheka kuti mukhalebe okhulupirika, n’cholinga choti mupitirizebe kukhala pakati pa anthu amene Mulungu wawaitana+ ndi kuwasankha,+ pakuti mukapitiriza kuchita zinthu zimenezi simudzalephera ngakhale pang’ono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena