Mateyu 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+ Machitidwe 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+ 1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+
21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+
29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+