Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma ngati satipulumutsa, dziwani mfumu kuti ife sititumikira milungu yanu, ndipo sitilambira fano limene mwaimika.”+

  • Malaki 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.”

      Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?”

      “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.

  • Maliko 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+

  • Luka 20:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iye anawauza kuti: “Chotero perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma za Mulungu kwa Mulungu.”+

  • Luka 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+

  • Aroma 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena