Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+ Tito 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+ 1 Petulo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,
7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+
3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+
13 Chifukwa cha Ambuye, gonjerani+ dongosolo lililonse lopangidwa ndi anthu:+ kaya mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,