Mateyu 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+ Maliko 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+ Luka 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anawauza kuti: “Chotero perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma za Mulungu kwa Mulungu.”+
21 Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.” Pamenepo iye anawauza kuti: “Ndiye perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara, koma za Mulungu, kwa Mulungu.”+
17 Pamenepo Yesu anati: “Perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma zinthu za Mulungu muzizipereka kwa Mulungu.”+ Ndipo iwo anadabwa naye kwambiri.+
25 Iye anawauza kuti: “Chotero perekani zinthu za Kaisara kwa Kaisara,+ koma za Mulungu kwa Mulungu.”+