Yohane 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+ Machitidwe 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+
19 Pamenepo Afarisi+ anayamba kuuzana kuti: “Apa ndiye mukudzionera nokha kuti palibiretu chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse lakhamukira kwa iye.”+
5 Ife tapeza kuti munthu uyu ndi wovutitsa kwabasi,+ ndipo akuyambitsa zoukira boma+ pakati pa Ayuda onse padziko lapansi kumene kuli anthu. Ndiponso ndi mtsogoleri wa gulu lampatuko wa Anazareti.+