Genesis 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+ Aefeso 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo. 1 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+
16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+
23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo.
3 Momwemonso+ inu akazi, muzigonjera+ amuna anu kuti ngati ali osamvera+ mawu akopeke,+ osati ndi mawu, koma ndi khalidwe lanu,+