1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
21 Ndipotu anakuitanirani ku moyo umenewu, pakuti ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+