Aroma 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye chifukwa chake Khristu anafa n’kukhalanso ndi moyo,+ kuti akhale Ambuye wa akufa+ ndiponso wa amoyo.+ Aefeso 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma polankhula zoona,+ tiyeni tikule m’zinthu zonse, kudzera m’chikondi,+ pansi pa iye amene ndi mutu,+ Khristu. Akolose 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzera mwa iyeyo, inu simukusowa kalikonse. Iye ndiye mwini ulamuliro wonse ndi mphamvu zonse.+
9 Ndiye chifukwa chake Khristu anafa n’kukhalanso ndi moyo,+ kuti akhale Ambuye wa akufa+ ndiponso wa amoyo.+
15 Koma polankhula zoona,+ tiyeni tikule m’zinthu zonse, kudzera m’chikondi,+ pansi pa iye amene ndi mutu,+ Khristu.