-
Zekariya 6:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndinakwezanso maso ndipo ndinaona magaleta anayi akubwera kuchokera pakati pa mapiri awiri. Mapiriwo anali amkuwa.
-