2 Mbiri 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anam’bweretsera kalata+ yochokera kwa mneneri Eliya.+ Kalatayo inati: “Yehova Mulungu wa Davide kholo lanu wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti sunayende m’njira za Yehosafati+ bambo ako, kapena m’njira za Asa+ mfumu ya Yuda,
12 Kenako anam’bweretsera kalata+ yochokera kwa mneneri Eliya.+ Kalatayo inati: “Yehova Mulungu wa Davide kholo lanu wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti sunayende m’njira za Yehosafati+ bambo ako, kapena m’njira za Asa+ mfumu ya Yuda,