2 Mafumu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova atatsala pang’ono kutenga Eliya+ mumphepo yamkuntho kupita naye kumwamba,+ Eliya ndi Elisa+ ananyamuka ku Giligala.+ 2 Mafumu 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene anali kuyenda n’kumalankhulana, anangoona galeta*+ lankhondo lowala ngati moto ndi mahatchi* owala ngati moto. Galeta ndi mahatchiwo zinadutsa pakati pawo n’kuwalekanitsa, ndipo Eliya anatengedwa mumphepo yamkuntho n’kukwera kumwamba.+
2 Yehova atatsala pang’ono kutenga Eliya+ mumphepo yamkuntho kupita naye kumwamba,+ Eliya ndi Elisa+ ananyamuka ku Giligala.+
11 Pamene anali kuyenda n’kumalankhulana, anangoona galeta*+ lankhondo lowala ngati moto ndi mahatchi* owala ngati moto. Galeta ndi mahatchiwo zinadutsa pakati pawo n’kuwalekanitsa, ndipo Eliya anatengedwa mumphepo yamkuntho n’kukwera kumwamba.+