2 Mafumu 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Elisa anayamba kupemphera+ kuti: “Inu Yehova, m’tseguleni maso+ chonde kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumiki uja, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo+ oyaka moto. Salimo 68:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+ Habakuku 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+
17 Kenako Elisa anayamba kupemphera+ kuti: “Inu Yehova, m’tseguleni maso+ chonde kuti aone.” Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumiki uja, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo+ oyaka moto.
17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+
8 Inu Yehova, kodi mwapsera mtima mitsinje?+ Kodi mkwiyo wanu wayakira nyanja+ pamene inu munakwera pamahatchi anu?+ Magaleta anu anabweretsa chipulumutso.+