Salimo 68:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+ Salimo 104:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+
17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali m’magulu a masauzande makumimakumi, ali m’magulu a masauzande osawerengeka.+Yehova walowa m’malo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+
3 Inu munamanga zipinda za m’mwamba pamadzi pogwiritsa ntchito mitanda,+Munapanga mitambo kukhala galeta lanu,+Mumayenda pamapiko a mphepo.+