Salimo 68:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali mʼmagulu a masauzande osawerengeka, ali mʼmagulu masauzandemasauzande.+ Yehova walowa mʼmalo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+
17 Magaleta ankhondo a Mulungu ali mʼmagulu a masauzande osawerengeka, ali mʼmagulu masauzandemasauzande.+ Yehova walowa mʼmalo oyera kuchokera kuphiri la Sinai.+