2 Mbiri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo patokha tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi khamu lalikulu limene likubwera kudzamenyana nafeli+ ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo patokha tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi khamu lalikulu limene likubwera kudzamenyana nafeli+ ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+