Oweruza 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipotu ine sindinakuchimwire, koma iwe ukundilakwira pomenyana nane. Yehova amene ndi Woweruza,+ aweruze lero pakati pa ana a Isiraeli ndi ana a Amoni.’” 1 Samueli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake+ mpaka kalekale chifukwa cha cholakwa ichi: Iye akudziwa+ kuti ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+ Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+
27 Ndipotu ine sindinakuchimwire, koma iwe ukundilakwira pomenyana nane. Yehova amene ndi Woweruza,+ aweruze lero pakati pa ana a Isiraeli ndi ana a Amoni.’”
13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake+ mpaka kalekale chifukwa cha cholakwa ichi: Iye akudziwa+ kuti ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+
6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+