1 Samueli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo iye anali kuwauza kuti:+ “Mukuchitiranji zinthu zoterezi?+ Chifukwatu anthu onse akundiuza zinthu zoipa zokhazokha zokhudza inu.+ Miyambo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+ ndipo usalakelake imfa yake.+ Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+ 1 Timoteyo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+
23 Ndipo iye anali kuwauza kuti:+ “Mukuchitiranji zinthu zoterezi?+ Chifukwatu anthu onse akundiuza zinthu zoipa zokhazokha zokhudza inu.+
11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+
20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+