Miyambo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wodzudzula munthu,+ patsogolo pake adzakondedwa kwambiri kuposa amene amakokomeza ndi lilime lake ponena zinthu zabwino za wina. Aefeso 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndipo musamachite nawo+ ntchito zosapindulitsa za mu mdima.+ M’malomwake, muzidzudzula ntchitozo.+ Tito 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa. Tito 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Umboni umenewu ndi woona. Chifukwa cha zimenezi, pitiriza kuwadzudzula mwamphamvu,+ kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba.+ Chivumbulutso 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+
23 Wodzudzula munthu,+ patsogolo pake adzakondedwa kwambiri kuposa amene amakokomeza ndi lilime lake ponena zinthu zabwino za wina.
11 ndipo musamachite nawo+ ntchito zosapindulitsa za mu mdima.+ M’malomwake, muzidzudzula ntchitozo.+
9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.
13 Umboni umenewu ndi woona. Chifukwa cha zimenezi, pitiriza kuwadzudzula mwamphamvu,+ kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba.+
19 “‘Onse amene ndimawakonda, ndimawadzudzula ndi kuwalanga.+ Choncho, khala wodzipereka ndipo ulape.+