Chivumbulutso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Choncho, kumbukira malo amene unali usanagwe, lapa+ ndi kuchita ntchito za poyamba. Ngati sutero, ndikubwera kwa iwe,+ ndipo ndidzachotsa choikapo nyale chako+ pamalo ake ngati sulapa. Chivumbulutso 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira+ ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira,+ ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka,+ ndidzabwera ngati mbala,+ ndipo sudzadziwa ngakhale pang’ono ola limene ndidzafike kwa iwe.+
5 “‘Choncho, kumbukira malo amene unali usanagwe, lapa+ ndi kuchita ntchito za poyamba. Ngati sutero, ndikubwera kwa iwe,+ ndipo ndidzachotsa choikapo nyale chako+ pamalo ake ngati sulapa.
3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira+ ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira,+ ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka,+ ndidzabwera ngati mbala,+ ndipo sudzadziwa ngakhale pang’ono ola limene ndidzafike kwa iwe.+