Luka 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chotero khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera+ nthawi zonse, kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyembekezeka kuchitika. Kutinso mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+ Afilipi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+
36 Chotero khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera+ nthawi zonse, kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyembekezeka kuchitika. Kutinso mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+
16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+