2 Akorinto 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inuyo mwavomereza kale, ngakhale kuti m’pang’ono pokha, kuti ifeyo ndife chifukwa choti mudzitamandire,+ ngati mmene inuyonso mudzakhalire chifukwa choti ifeyo tidzadzitamandire m’tsiku la Ambuye wathu Yesu.+ 1 Atesalonika 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?
14 Inuyo mwavomereza kale, ngakhale kuti m’pang’ono pokha, kuti ifeyo ndife chifukwa choti mudzitamandire,+ ngati mmene inuyonso mudzakhalire chifukwa choti ifeyo tidzadzitamandire m’tsiku la Ambuye wathu Yesu.+
19 Kodi chiyembekezo chathu, kapena chimwemwe chathu n’chiyani? Inde, mphoto*+ yathu yoinyadira pamaso pa Ambuye wathu Yesu, pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake n’chiyani? Si inu amene kodi?