Mateyu 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chotero khalanibe maso+ chifukwa simukudziwa tsiku kapena ola lake.+ Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ pakuti simukudziwa pamene nthawi yoikidwiratu idzafika.+