Mateyu 24:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chotero khalanibe maso chifukwa simukudziwa tsiku limene Ambuye wanu adzabwere.+ Mateyu 24:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 mbuye wa kapoloyo adzabwera pa tsiku limene iye sakuyembekezera ndi pa ola+ limene sakulidziwa. Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ pakuti simukudziwa pamene nthawi yoikidwiratu idzafika.+