Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma ine ndinati: “Ndangovutika pachabe.+ Mphamvu zanga ndangoziwonongera zinthu zopanda pake ndi zachabechabe.+ Ndithu, Yehova ndiye amene adzandiweruze+ ndipo Mulungu wanga ndiye amene adzandipatse mphoto yanga.”+

  • Agalatiya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndinapita kumeneko chifukwa ndinauzidwa m’masomphenya kuti ndipiteko.+ Ndipo ndinafotokozera+ amuna odalirika, uthenga wabwino umene ndikuulalikira kwa anthu a mitundu ina. Ndinachita zimenezo chifukwa ndinkaopa kuti mwina ndinali kuthamanga+ popanda phindu, kapena ndinali nditathamanga kale pachabe.+ Koma ndinawafotokozera zimenezi kumbali.

  • 1 Atesalonika 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiye chifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinamutuma kuti ndidziwe za kukhulupirika+ kwanu, kuti mwina mwa njira ina, Woyesayo+ angakhale atakuyesani, ndipo ntchito imene tinagwira mwakhama ingakhale itapita pachabe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena