Afilipi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+ 1 Atesalonika 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiye chifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinamutuma kuti ndidziwe za kukhulupirika+ kwanu, kuti mwina mwa njira ina, Woyesayo+ angakhale atakuyesani, ndipo ntchito imene tinagwira mwakhama ingakhale itapita pachabe.+
16 Muchite zimenezi pamene mukupitirizabe kugwira mwamphamvu mawu amoyo,+ kuti ndikakhale ndi chifukwa chosangalalira m’tsiku la Khristu,+ poona kuti sindinathamange pachabe, kapena kuchita khama pachabe.+
5 Ndiye chifukwa chake pamene sindinathenso kupirira, ndinamutuma kuti ndidziwe za kukhulupirika+ kwanu, kuti mwina mwa njira ina, Woyesayo+ angakhale atakuyesani, ndipo ntchito imene tinagwira mwakhama ingakhale itapita pachabe.+