Salimo 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+ Salimo 140:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+
23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+
12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+