Chivumbulutso 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka, ndidzabwera ngati wakuba+ ndipo sudzadziwa ngakhale pangʼono ola limene ndidzafike kwa iwe.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, ptsa. 3-4 Nsanja ya Olonda,5/1/2009, ptsa. 13-145/15/2003, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 31-32, 55-56
3 Choncho, pitiriza kukumbukira zimene unalandira ndi zimene unamva. Pitiriza kuzitsatira ndipo ulape.+ Ndithudi, ukapanda kudzuka, ndidzabwera ngati wakuba+ ndipo sudzadziwa ngakhale pangʼono ola limene ndidzafike kwa iwe.+
3:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, ptsa. 3-4 Nsanja ya Olonda,5/1/2009, ptsa. 13-145/15/2003, tsa. 17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 31-32, 55-56