Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 52:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+

  • Aroma 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano ndikukudandaulirani abale, kuti musamale ndi anthu amene amayambitsa magawano+ ndi kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi chiphunzitso+ chimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+

  • 2 Atesalonika 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano tikukulangizani+ abale m’dzina la Ambuye Yesu Khristu, kuti mupewe+ m’bale aliyense woyenda mosalongosoka+ komanso mosagwirizana ndi mwambo umene tinakupatsani.+

  • 2 Timoteyo 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 ndiponso ooneka ngati odzipereka kwa Mulungu+ koma amakana kuti mphamvu ya kudziperekako iwasinthe.+ Anthu amenewa uwapewe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena