8 Azisamalira ziwiya zonse+ za pachihema chokumanako, monga gawo limodzi la ntchito za ana a Isiraeli zimene a fuko la Leviwo aziwagwirira potumikira pachihema chopatulika.+
7 Komanso, Mfumu Koresi inabweretsa ziwiya za nyumba ya Yehova.+ Ziwiyazo n’zimene Nebukadinezara anatenga ku Yerusalemu+ n’kukaziika m’kachisi wa mulungu wake.+