Ekisodo 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nawonso ansembe amene amayandikira kwa Yehova kawirikawiri adziyeretse,+ kuti mkwiyo wa Yehova usawayakire.”+ Yesaya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+
22 Nawonso ansembe amene amayandikira kwa Yehova kawirikawiri adziyeretse,+ kuti mkwiyo wa Yehova usawayakire.”+
11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+