-
Ezara 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Komanso, ziwiya zagolide ndi zasiliva+ zimene Nebukadinezara anazitenga m’kachisi wa Mulungu yemwe anali ku Yerusalemu, n’kupita nazo kukachisi wa ku Babulo,+ mfumu Koresi+ inazichotsa m’kachisi wa ku Babuloyo. Ndiyeno zinaperekedwa kwa Sezibazara,+ munthu amene Koresi anamuika kukhala bwanamkubwa.+
-