Hagai 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda, Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse. Choncho iwo anapita kukagwira ntchito panyumba ya Yehova wa makamu, Mulungu wawo.+ Hagai 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde, kauze Zerubabele,+ mwana wa Salatiyeli+ bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse kuti,
14 Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda, Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse. Choncho iwo anapita kukagwira ntchito panyumba ya Yehova wa makamu, Mulungu wawo.+
2 “Chonde, kauze Zerubabele,+ mwana wa Salatiyeli+ bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse kuti,