Ezara 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati yemwe anabweretsa ziwiyazo n’kuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.+
8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati yemwe anabweretsa ziwiyazo n’kuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.+