Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, Yehova analimbikitsa+ mtima wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa+ mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti:

  • Ezara 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno atsogoleri+ a mabanja a fuko la Yuda, la Benjamini, ansembe, ndi Alevi, aliyense amene Mulungu woona analimbikitsa mtima wake,+ ananyamuka kuti apite kukamanganso nyumba ya Yehova,+ yomwe inali ku Yerusalemu.

  • Zekariya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Afilipi 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti Mulungu amachita zinthu m’njira imene imamusangalatsa. Iye amalimbitsa zolakalaka zanu+ kuti muchite zinthu zonse zimene iye amakonda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena