Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno ndinadzuka usiku pamodzi ndi amuna angapo amene ndinali nawo. Sindinauze munthu aliyense+ zimene Mulungu wanga anali kuika mumtima mwanga zoti ndichitire Yerusalemu,+ ndipo ndinalibe chiweto chilichonse kupatulapo chiweto chimene ndinakwerapo.

  • Afilipi 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti Mulungu amachita zinthu m’njira imene imamusangalatsa. Iye amalimbitsa zolakalaka zanu+ kuti muchite zinthu zonse zimene iye amakonda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena