Mlaliki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yong’amba+ ndi nthawi yosoka.+ Nthawi yokhala chete+ ndi nthawi yolankhula.+ Amosi 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
13 Choncho, munthu wozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo chifukwa chakuti idzakhala nthawi yoopsa.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+