Salimo 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitirani Ziyoni zabwino mwa kukoma mtima kwanu.+Ndipo mangani mpanda wa Yerusalemu.+ Salimo 122:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu, anthu inu.+Amene amakukonda, mzinda iwe, sadzakhala ndi nkhawa iliyonse.+
6 Pemphererani mtendere wa Yerusalemu, anthu inu.+Amene amakukonda, mzinda iwe, sadzakhala ndi nkhawa iliyonse.+