Salimo 102:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova adzamangadi Ziyoni.+Iye ayenera kuonekera mu ulemerero wake.+ Yesaya 62:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+
62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+