Salimo 137:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilime langa limamatire m’kamwa mwanga+Ngati sindingakukumbukire,+Ngati sindingakweze iwe YerusalemuPamwamba pa chilichonse chimene chimandikondweretsa.+ Zekariya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova adzatenga Yuda kukhala gawo lake m’dziko loyera,+ ndipo adzasankha Yerusalemu.+
6 Lilime langa limamatire m’kamwa mwanga+Ngati sindingakukumbukire,+Ngati sindingakweze iwe YerusalemuPamwamba pa chilichonse chimene chimandikondweretsa.+