Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Numeri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+