Numeri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye wagwada pansi, wagona pansi ngati mkango,Ngati mkango, ndani angayese kumʼdzutsa? Amene akudalitsa iwe adzadalitsidwa,Ndipo amene akukutemberera, adzatembereredwa.”+
9 Iye wagwada pansi, wagona pansi ngati mkango,Ngati mkango, ndani angayese kumʼdzutsa? Amene akudalitsa iwe adzadalitsidwa,Ndipo amene akukutemberera, adzatembereredwa.”+