Numeri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+
9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+