Genesis 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mafuko akutumikire ndipo mitundu ya anthu ikugwadire.+ Ukhale mbuye wa abale ako, ndipo ana a mayi ako akugwadire.+ Aliyense wokutemberera atembereredwe, ndipo aliyense wokudalitsa adalitsidwe.”+
29 Mafuko akutumikire ndipo mitundu ya anthu ikugwadire.+ Ukhale mbuye wa abale ako, ndipo ana a mayi ako akugwadire.+ Aliyense wokutemberera atembereredwe, ndipo aliyense wokudalitsa adalitsidwe.”+