2 Samueli 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Mefiboseti anauza mfumu kuti: “Musiyeni atenge munda wonsewo,+ popeza kuti tsopano inu mbuyanga mfumu mwabwerera kunyumba yanu mu mtendere.” Salimo 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitirani Ziyoni zabwino mwa kukoma mtima kwanu.+Ndipo mangani mpanda wa Yerusalemu.+
30 Pamenepo Mefiboseti anauza mfumu kuti: “Musiyeni atenge munda wonsewo,+ popeza kuti tsopano inu mbuyanga mfumu mwabwerera kunyumba yanu mu mtendere.”