Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose+ mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli m’chipululu.

  • 2 Mbiri 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho anagwirizana kuti alengeze+ zimenezi mu Isiraeli yense kuyambira ku Beere-seba+ mpaka ku Dani,+ ndipo auze anthuwo kuti abwere ku Yerusalemu adzachite pasika kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli, chifukwa m’mbuyomo, iwo sanali kusonkhana onse pamodzi+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena