Numeri 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+ Yesaya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+
51 Pa nthawi yosamutsa chihema chopatulika, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, iwo ndiwo azimanga chihemacho. Aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+
11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+