Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+ Numeri 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Isiraeli asadzayandikirenso chihema chokumanako, kuti angadzachimwe n’kufa.+ 1 Samueli 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero Mulungu anakantha anthu a ku Beti-semesi,+ chifukwa anayang’anitsitsa likasa la Yehova. Anakantha anthu 70 [[anthu 50,000]]* pakati pawo, ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anakantha anthuwo koopsa.+
10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+
19 Chotero Mulungu anakantha anthu a ku Beti-semesi,+ chifukwa anayang’anitsitsa likasa la Yehova. Anakantha anthu 70 [[anthu 50,000]]* pakati pawo, ndipo anthu anayamba kulira chifukwa Yehova anakantha anthuwo koopsa.+