Yesaya 49:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe Isiraeli ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndidzaonetsera kukongola kwanga pa iwe.”+ Yohane 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yudasi atatuluka, Yesu anati: “Tsopano Mwana wa munthu walemekezedwa,+ ndipo Mulungu walemekezedwa kudzera mwa iye. 2 Atesalonika 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Adzatero pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero mogwirizana ndi oyera ake.+ Pa tsiku limenelo, onse amene anakhulupirira mwa iye, adzamusirira ndi kumuyang’anitsitsa, chifukwa pakati panu, munakhulupirira umboni umene tinapereka.
3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe Isiraeli ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndidzaonetsera kukongola kwanga pa iwe.”+
31 Yudasi atatuluka, Yesu anati: “Tsopano Mwana wa munthu walemekezedwa,+ ndipo Mulungu walemekezedwa kudzera mwa iye.
10 Adzatero pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero mogwirizana ndi oyera ake.+ Pa tsiku limenelo, onse amene anakhulupirira mwa iye, adzamusirira ndi kumuyang’anitsitsa, chifukwa pakati panu, munakhulupirira umboni umene tinapereka.