-
2 Atesalonika 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Zimenezi zidzachitika pa nthawi imene adzabwere kudzalandira ulemerero limodzi ndi oyera ake. Pa tsiku limenelo, onse amene anamukhulupirira adzamuyangʼanitsitsa mwachidwi, chifukwa munakhulupirira umboni umene tinapereka kwa inu.
-